Genesis 29:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Labani anati kwa iye, Etu, iwe ndiwe pfupa langa ndi thupi langa. Ndipo anakhala naye nthawi ya mwezi umodzi.

Genesis 29

Genesis 29:11-22