Genesis 29:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali pamene Labani anamva mbiri ya Yakobo mwana wa mlongo wace, iye anathamangira kukakomana naye namfungatira, nampsompsona, namlowetsa m'nyumba mwace. Ndipo iye anamfotokozera Labani zinthu zonsezo.

Genesis 29

Genesis 29:5-14