Genesis 29:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Labani anati kwa Yakobo, Cifukwa iwe ndiwe mbale wanga, kodi udzanditumikira ine kwacabe? Undiuze ine, malipiro ako adzakhala otani?

Genesis 29

Genesis 29:9-23