Ezekieli 9:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati kwa iwo, Muipse nyumbayi ndi kudzaza mabwalo ndi ophedwa, mukani. Ndipo anaturuka, nakantha m'mudzimo.

Ezekieli 9

Ezekieli 9:2-9