Ezekieli 9:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

iphanitu nkhalamba, mnyamata ndi namwali, makanda, ndi akazi; koma musayandikira munthu ali yense ali naco cizindikilo, ndipo muyambe pa malo anga opatulika, Pamenepo anayamba ndi akuluwo anali pakhomo pa nyumba.

Ezekieli 9

Ezekieli 9:1-11