Ezekieli 9:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, alimkukantha iwo, nditatsala ine, ndinagwa nkhope yanga pansi, ndi kupfuula, ndi kuti, Kalanga ine. Ambuye Mulungu! kodi mudzaononga otsala onse a Israyeli pakutsanulira ukali wanu pa Yerusalemu?

Ezekieli 9

Ezekieli 9:1-11