Ezekieli 48:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi ku mbali ya kumwela ayese zikwi zinai mphambu mazana asanu, ndi zipata zitatu: cipata cimodzi ca Simeoni, cipata cimodzi ca Isakara, cipata cimodzi ca Zebuloni;

Ezekieli 48

Ezekieli 48:30-35