Ezekieli 48:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ku mbali ya kumadzulo zikwi zinai mphambu mazana asanu, ndi zipata zace zitaru; cipata cimodzi ca Gadi, cipata cimodzi ca Aseri, cipata cimodzi ca Nafitali.

Ezekieli 48

Ezekieli 48:30-35