Ezekieli 46:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anaturukira nane ku bwalo lakunja, nandipititsa ku ngondya zinai za bwaloli; ndipo taonani, m'ngondya monse munali bwalo.

Ezekieli 46

Ezekieli 46:16-24