Ezekieli 46:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

M'ngondya zinai za bwalo munali mabwalo ocingika, m'litali mwace mikono makumi anai, kupingasa kwace makumi atatu; awa anai m'ngondyazi analingana muyeso wace.

Ezekieli 46

Ezekieli 46:21-24