Ezekieli 46:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati kwa ine, Pano ndipo ansembe aziphikira nsembe yoparamula, ndi nsembe yaucimo; kumenenso azioca mikate ya ufa wa nsembe, kuti asaturuke nazo ku bwalo lakunja ndi kupatulikitsa anthu,

Ezekieli 46

Ezekieli 46:11-24