Ezekieli 44:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza anawatumikira pamaso pa mafano ao, nakhala cokhumudwitsa ca mphulupulu ca nyumba ya Israyeli, cifukwa cace ndawakwezera dzanja langa, ati Ambuye Yehova; ndipo adzasenza mphulupulu yao.

Ezekieli 44

Ezekieli 44:6-22