Ezekieli 44:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma adzakhala atumiki m'malo anga opatulika, akuyang'anira ku zipata za kacisi, ndi kutumikira m'kacisimo, aziwaphera anthu nsembe yopsereza, ndi nsembe yophera naime pamaso pao kuwatumikira.

Ezekieli 44

Ezekieli 44:7-21