Ezekieli 36:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace nena kwa nyumba ya Israyeli, Atero Ambuye Yehova, Sindicicita ici cifukwa ca inu, nyumba ya Israyeli, koma cifukwa ca dzina langa loyera munaliipsalo pakati pa amitundu, kumene mudamukako.

Ezekieli 36

Ezekieli 36:21-24