Ezekieli 36:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ndinawaleka cifukwa ca dzina langa loyera, limene a nyumba ya Israyeli adalidetsa pakati pa amitundu, kumene adarakako,

Ezekieli 36

Ezekieli 36:11-30