Ezekieli 19:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Unaturukanso moto ku ndodo za ku nthambi zace, unatha zipatso zace; m'mwemo ulibe ndodo yolimba ikhale ndodo yacifumu ya kucita ufumu. Iyi ndi nyimbo idzakhala nyimbo ya maliro.

Ezekieli 19

Ezekieli 19:11-14