Ezekieli 19:13-14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

13. Ndipo tsopano waokedwa m'cipululu m'dziko louma ndi la ludzu.

14. Unaturukanso moto ku ndodo za ku nthambi zace, unatha zipatso zace; m'mwemo ulibe ndodo yolimba ikhale ndodo yacifumu ya kucita ufumu. Iyi ndi nyimbo idzakhala nyimbo ya maliro.

Ezekieli 19