Ezekieli 10:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinapenya, ndipo taonani, ku thambo lokhala pamwamba pa mitu ya akerubi kudaoneka ngati mwala wasafiro, ngati maonekedwe a cifaniziro ca mpando wacifumu pamwamba pao.

Ezekieli 10

Ezekieli 10:1-4