Ezekieli 9:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo taonani, munthu wobvala bafutayo, wokhala ndi zolembera nazo m'cuuno mwace, anabweza mau, ndi kuti, Ndacita monga munandilamulira ine.

Ezekieli 9

Ezekieli 9:1-11