Ezekieli 10:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova analankhula ndi munthu wobvala bafuta, nati, Lowa pakati pa njingazi pansi pa kerubi, nudzaze manja ako makara a moto ocokera pakati pa akerubi, nuwamwaze pamwamba pa mudzi. Nalowa, ndiri cipenyere ine.

Ezekieli 10

Ezekieli 10:1-10