Ezekieli 1:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panamveka mau pamwamba pa thambolo linali pamwamba pa mitu yao; pakuima izi zinagwetsa mapiko ao.

Ezekieli 1

Ezekieli 1:21-26