Ezekieli 1:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakuyenda izi ndinamva mkokomo wa mapiko ao, ngati mkokomo wa madzi akulu, ngati mau a Wamphamvuyonse, phokoso lakusokosera ngati phokoso la ankhondo; pakuima zinagwetsa mapiko ao.

Ezekieli 1

Ezekieli 1:19-28