Ezekieli 1:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi pamwamba pa thambo linali pamitu pao panali cifaniziro ca mpando wacifumu, maonekedwe ace ngati mwala wa safiro; ndipo pa cifaniziro ca mpando wacifumu panali cifaniziro ngati maonekedwe ace a munthu wokhala pamwamba pace.

Ezekieli 1

Ezekieli 1:23-28