Eksodo 2:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo atakula mwanayo, anapita naye kwa mwana wamkazi wa Farao, ndipo iye anakhala mwana wace. Ndipo anamucha dzina lace Mose, nati, Cifukwa ndinambvuula m'madzi.

Eksodo 2

Eksodo 2:6-12