Eksodo 2:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali masiku amenewo, atakula Mose, kuti anaturukira kukazonda abale ace, napenya akatundu ao; ndipo anaona munthu M-aigupto ali kukantha Mhebri, wa abale ace.

Eksodo 2

Eksodo 2:2-21