Eksodo 2:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mwana wamkazi wa Farao ananena naye, Pita naye mwana uyu, ndi kundiyamwitsira iye, ndidzakupatsa mphotho yako. Ndipo mkaziyo anatenga mwanayo, namyamwitsa,

Eksodo 2

Eksodo 2:1-16