Deuteronomo 28:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mtundu wa anthu umene simudziwa udzadya zipatso za nthaka yanu ndi nchito zanu zonse; ndipo mudzakhala wopsinjika ndi wophwanyika masiku onse;

Deuteronomo 28

Deuteronomo 28:25-35