Deuteronomo 2:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pamenepo tinabwerera, ndi kuyenda kumka kucipululu, kutsata njira ya Nyanja Yofiira, monga Yehova adanena ndi ine; ndipo tinapaza phiri la Seiri masiku ambiri.

2. Ndipo Yehova ananena ndi ine, ndi kuti,

Deuteronomo 2