Deuteronomo 2:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo tinabwerera, ndi kuyenda kumka kucipululu, kutsata njira ya Nyanja Yofiira, monga Yehova adanena ndi ine; ndipo tinapaza phiri la Seiri masiku ambiri.

Deuteronomo 2

Deuteronomo 2:1-7