Deuteronomo 3:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo tinatembenuka, ndi kubwera kumka njira ya ku Basana; ndipo Ogi mfumu ya Basana anaturuka kukomana nafe, kugwirana nafe nkhondo, iye ndi anthu ace onse, ku Edrei.

Deuteronomo 3

Deuteronomo 3:1-11