Danieli 11:44-45 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

44. Koma mbiri yocokera kum'mawa ndi kumpoto idzambvuta; nadzaturuka iye ndi ukali waukuru kupha ndi kuononga konse ambiri.

45. Ndipo adzamanga mahema a nyumba yacifumu yace pakati pa nyanja yamcere ndi phiri lopatulika lofunika; koma adzafikira cimariziro cace wopanda wina wakumthandiza.

Danieli 11