Danieli 10:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ndidzakufotokozera colembedwa pa lemba la coonadi; ndipo palibe wina wakudzilimbikitsa pamodzi ndi ine, kutsutsana ndi aja, koma Mikaeli kalonga wanu.

Danieli 10

Danieli 10:13-21