Danieli 10:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anati, Kodi udziwa cifukwa coti ndakudzera? ndipo tsopano ndibwerera kulimbana ndi kalonga wa Perisiya; ndipo pomuka ine, taonani, adzadza kalonga wa Helene.

Danieli 10

Danieli 10:16-21