Danieli 10:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati, Munthu wokondedwatu iwe, Usaope, mtendere ukhale nawe; limbika, etu limbika. Ndipo pamene ananena ndi ine ndinalimbikitsidwa, ndinati, Anene mbuye wanga; pakuti mwandilimbikitsa.

Danieli 10

Danieli 10:11-21