Danieli 11:45 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adzamanga mahema a nyumba yacifumu yace pakati pa nyanja yamcere ndi phiri lopatulika lofunika; koma adzafikira cimariziro cace wopanda wina wakumthandiza.

Danieli 11

Danieli 11:43-45