Danieli 11:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma kumalo kwace idzacitira ulemu mulungu wa malinga; ndi mulungu amene makolo ace sanaudziwa, adzaulemekeza ndi golidi, ndi siliva, ndi miyala ya mtengo wace, ndi zinthu zofunika.

Danieli 11

Danieli 11:34-39