Danieli 11:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adzacita molimbana ndi malinga olimba koposa, pomthandiza mulungu wacilendo; ali yense wombvomereza adzamcurukitsira ulemu, nadzawacititsa ufumu pa ambiri, nadzagawa dziko mwa mtengo wace.

Danieli 11

Danieli 11:34-45