Danieli 11:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo sidzasamalira milungu ya makolo ace, kapena coikhumba akazi, kapena kusamalira milungu iri yonse; pakuti idzadzikuza koposa onse.

Danieli 11

Danieli 11:33-38