Amosi 3:3-5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. Kodi awiri adzayenda pamodzi asanapanganiranetu?

4. Kodi mkango udzabangula m'nkhalango wosakhala nayo nyama? Kodi msona wa mkango udzalira m'ngaka mwace usanagwire kanthu?

5. Kodi mbalame idzakodwa mumsampha pansi popanda msampha woichera? Kodi msampha ufamphuka pansi wosakola kanthu?

Amosi 3