Amosi 3:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi mkango udzabangula m'nkhalango wosakhala nayo nyama? Kodi msona wa mkango udzalira m'ngaka mwace usanagwire kanthu?

Amosi 3

Amosi 3:3-5