Amosi 4:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tamverani mau awa, inu ng'ombe zazikazi za ku Basana, zokhala m'phiri la Samariya, zosautsa aumphawi, zopsinja osowa, zonena kwa ambuyao, Bwerani naco, timwe.

Amosi 4

Amosi 4:1-4