Amosi 3:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzakantha nyumba ya nyengo yacisanu, pamodzi ndi nyumba ya nyengo yadzuwa; ndi nyumba zaminyanga zidzaonongeka; ndi nyumba zazikuruzo zidzatha, ati Yehova.

Amosi 3

Amosi 3:14-15