Amosi 3:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti tsiku lakumlanga Israyeli cifukwa ca zolakwa zace, ndidzalanganso maguwa a nsembe a ku Beteli; ndi nyanga za guwa la nsembe zidzadulidwa, nizidzagwa pansi.

Amosi 3

Amosi 3:5-15