Amosi 2:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinakukwezani kucokera m'dziko la Aigupto, ndi kukutsogolerani zaka makumi anai m'cipululu, kuti mulandire dziko la Aamori likhale colowa canu.

Amosi 2

Amosi 2:3-16