Amosi 2:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinaukitsa mwa ana anu aneneri, ndi mwa anyamata anu Anaziri. Si momwemo, inu ana a Israyeli, ati Yehova?

Amosi 2

Amosi 2:2-16