2 Samueli 3:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali nkhondo nthawi yaitali pakati pa nyumba ya Sauli ndi nyumba ya Davide. Koma Davide analimba cilimbire, ndi nyumba ya Sauli inafoka cifokere.

2 Samueli 3

2 Samueli 3:1-6