2 Samueli 3:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana a Davide anabadwira ku Hebroni. Mwana woyamba ndiye Amnoni, wa Ahinoamu wa ku Jezreeli;

2 Samueli 3

2 Samueli 3:1-10