2 Samueli 2:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ananyamula Asaheli namuika m'manda a atate wace ali ku Betelehemu. Ndipo Yoabu ndi anthu ace anacezera kuyenda usiku wonse, ndipo kudawacera ku Hebroni.

2 Samueli 2

2 Samueli 2:31-32