2 Samueli 23:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati, Ndisacite ici ndi pang'ono ponse, Yehova; ndimwe kodi mwazi wa anthu awa ana pitawa ndi kutaya moyo wao? Cifukwa cace iye anakana kumwa. Izi anazicita ngwazi zitatuzi.

2 Samueli 23

2 Samueli 23:15-20