2 Samueli 23:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abisai, mbale wa Yoabu, mwana wa Zeruya, anali wamkuru wa atatuwa. Iye natukula mkondo wace pa anthu mazana atatu nawapha, natenga dzina iye mwa atatuwa.

2 Samueli 23

2 Samueli 23:12-22